Traktat Chichewa (Malawi)
Glücklich sind...
ist ein evangelistisches Traktat, welches die Kernaussagen der Bibel – die Gute Nachricht von Jesus Christus – zusammenfasst. Die Verteilschrift gibt Antwort auf oft gestellte Fragen und lädt zu einer persönlichen Begegnung mit Jesus Christus ein bzw. zu einer persönlichen Beziehung mit ihm. Sämtliche Aussagen werden mit Bibelstellen belegt und regen zum ausführlicheren Bibellesen an. Eine Einladung an alle, die Gott noch nicht kennen und eine Hilfe für Christen, die suchende Menschen zu Jesus führen wollen. Das Verteilheft ist durch seinen stabilen Umschlag mehr Buch als Traktat und passt in jede Hosentasche...
Odala ali iwo…
Munthu wayesa koma walephera kupeza tanthauzo lenileni la moyo. Munthu wayesetsa kufunafuna kuti apeze Mulungu kudzeza muchipembedzo kapena kudzera mukuchita ntchito zachifundo koma walephera kwambiri. Kufuna Mulungu kudzera mu chilengedwe kapena mu kafukufuku ndi nzeru za anthu sizidapindule. Anthu amaganiza kuti Mulungu ali kutali nawo, ndipo chiyembekezo chonse ndi mtendere mkati mwa munthu zichoka. Anthu a dziko lapansi ali kufunafuna Mulungu ndipo ena amadziwa zoti ali kufuna Mulungu koma ena sadziwa. Munthu ali wosautsidwa chifukwa adataya moyo wosatha ndipo ali kuyesayesa kuti alimikize pompho lomwe lilipo pakati pa iye ndi Mlengi wake.
Dzanja la Mlengi lidaika chizindikiro cholembedwa pa munthu aliyense. Tonse tidalengedwa ndi cholinga. Kuzindikira chomwe uli, kapena kudziwa chomwe uyenera kukwaniritsa si zolinga zokhazo za moyo wa munthu, koma tanthauzo lenileni la moyo wa munthu lipezeka mwa Mulungu yekha.
Palibe yemwe angafune kudziwa za moyo osafunsa za Mulungu. Aliyense akumana ndi nyengo limene limupangitsa kufuna yankho ku funso limeneli.
Mulungu adadzala moyo
wosatha mumtima mwa
munthu. ( M l a l i k i 3 : 1 1 )
Leseprobe/Extract
Kusindikiza kwachiwiri mu chingerezi
ISBN 978-3-942632-64-5
Art.-Nr.: 812664000
Zu beziehen bei:
SCM-Shop im ICMedienhaus:
Tel.-Nr. +49(0)7031-7414-177, Fax: (-119), E-Mail:
bestellen@scm-shop.de oder über Ihre Buchhandlung
Download als Ebook: